God is a mystery that is experienced best when enlightened. |
Mulungu ndi mphmvu yodabwisa imene imaveka ukazindikila |
We can only say that it is good to live in God. |
Titha kunena kuti m'kwabwino kukhala mwa ambuye |
It is better to be enlightened than not enlightened. |
M'kwabwino kuzindikila kusiyana ndikusazindikila |
Enlightenment is the deeper purpose of life. |
Kuzindikila nde cholinga chachikulu cha moyo |
Through enlightenment, we reach the kingdom of God. |
Kudzela kuzindikila,timafikila kumwamba |
Enlightenment means inner peace, inner happiness and all-encompassing love for all beings. |
Kuzindikila kumatanthauza mtendere wamumtima,chimwemwe chamumtima koma kwakukulu chikondi cha zinthu zonse |
An enlightened person lives in God. |
Munthu ozindikila amakhala mwa ambuye |
He or she sees God as a kind of light in the world. |
Iye amaona Mulungu ngati kuwala kwa dziko |
He or she feels God in him or herself and around him or herself. |
iye amawona kupezeka kwa Mulungu mwa iye |
He or she feels God as inner happiness, inner peace and inner strength and is aware that he or she is in a higher truth that can only be described as universal love. |
iye amaona mulungu ngati chimwemwe chamuntima,mtendele wamumtima,mphamvu zamumtima ndi ndiozindikila kuti iye ndi chilungamo chachikulu chomwe chitha kufotokozeledwa kuti chikondi chachikulu |
In each of the major religions, there are varied definitions of God. |
Muzipembezo zikuluzikulu zilizonse,muli matanthauzo a mulungu osiyanasiyana |
In the religions we also find the personal and abstract term of God. |
muchipembezo timapezamo tanthauzo la mulungu mwa umunthu komanso tanthauzo lolemekezeka |
Many enlightened mystics think of God as a person and some others as a higher dimension in the cosmos. |
Anthu ozindikila ambili amaganiza kuti mulungu ndi munthu pamene ena amangowona ngati ndi chinthu chili mlengalenga |
In Buddhism and in Hinduism the abstract term of God dominates. |
Muchipembezo chachi Budda komanso chihindu tanthauzo la mulungu ndi lapadeladela |
In Buddhism, the highest principle is called Nirvana and in Hinduism it’s called Brahman. |
Mu Chipembezo cha Budda,mulungu wawo amamutcha Nirvana pamene muchipembezo chachi Hindu amati Brahman |
Jesus referred to God as father. |
Yesu anati Mulungu ndi tate |
Moses referred to God more in an abstract fashion. |
Mose amakamba mulungu mwapadela |
His central definition of God was described with the words “I am.” |
Dzina la Mulungu linkatanthauzidwa kwambili kuti "ine ndine" |
These words refer to God as a happy state of being where one experiences enlightenment. |
Mawu amenewa amatanthauza ngati mulungu ndi kumva kusangalala komwe kumabwelesa kuzindikila |
In the words “I am” we find the main way to enlightenment. |
Mu mawu akuti "ine ndine" timapezamo kuzindikila |
People need to develop a cosmic consciousness, a consciousness of the unity of all things. |
anthu ayenela kumvesesa zakumwamba,kumvesesa zakugwilizana kwa zinthu |
Thus the ego consciousness is lost. |
choncho kudzikhulupilira kodzikweza kumasowa |
Then one experiences pure consciousness, is one with everything and can only say: “I am.” |
Ndipo pamenepo munthu amadzikhulupilira mwabwino,ndi munthu wachina chilichose amene atha kunena kuti:"ine ndine" |
He or she cannot say “I am so and so.” |
Iye sanganena kuti "ine ndi wakuti wakuti" |
He or she identifies with everything and everyone and is personally nothing and is simply consciousness. |
iye amadziwika ndi chilichose komanso wina aliyense ndipo ndiozichepesa |
God as a being who can take action helps us along the spiritual way. |
Mulungu amene angapange zinthu amatithandiza mmoyo wathu wa uzimu |
All enlightened beings are an incarnation of God. |
Anthu ozindikila nde mokhala mwa Mulungu |
If you connect with God or an enlightened being daily, you will be lead in the light. |
Ukalumikizana ndi Mulungu kapena kuzindikila tsiku lililonse,umatsogoleledwa mukuwunika |